Buku la Mamasulidwa a kwa Omangidwa limapereka zinthu zapadera zoperekera machiritso ndi ufulu. Limapereka makiyi ogwiritsira ntchito mphamvu ya mtanda kutenga 'ufulu wa ulemerero wa ana a Mulungu' (Aroma 8:21 ). Mapemphero ndi zolengeza mu masamba awa zayesedwa m'makontinenti asanu ndi limodzi. Zatsimikizira kuthekera kothandiza kumasula anthu, kuswa linga la mibadwo ndi kuwamasula kukhala mboni zolimba mtima ndi zogwira mtima za mphamvu yopulumutsa ya Khristu.
Bitte wählen Sie Ihr Anliegen aus.
Rechnungen
Retourenschein anfordern
Bestellstatus
Storno



![Learning to Lead at the Feet of Jesus [Spanish] Aprendiendo a Liderar a los Pies de Jesús Learning to Lead at the Feet of Jesus [Spanish] Aprendiendo a Liderar a los Pies de Jesús](https://bilder.buecher.de/produkte/75/75636/75636700m.jpg)



