Kukhalapo kwa Mulungu n'kofunika!
Kukhalapo kwa Mulungu n'kofunika kwambiri pa miyoyo yathu, ndipo tiyenera kulikufuna ndi mitima yathu yonse. Sititha konse, m'njira iliyonse, kuchepetsa kufunika kwa kukhalapo kwa Mulungu pa kuyenda kwathu naye. Tiyenera nthawi zonse kukhala tikulifunafuna kukhalapo kwa Mulungu.
Kukhala ndi kukhalapo kodzozedwa pamodzi nanu, n'kukhala ndi Kukhalapo Kopatulika kwa Mulungu m'moyo mwanu. Ndi pemphero langa kuti mtima wanu utsitsimuke kulakalaka kukhalapo kwa Mulungu kwamtengo wapatali pamene mukuwelenga buku lodabwitsali lolemba Dag Heward-Mills.
Dieser Download kann aus rechtlichen Gründen nur mit Rechnungsadresse in A, B, CY, CZ, D, DK, EW, E, FIN, F, GR, H, IRL, I, LT, L, LR, M, NL, PL, P, R, S, SLO, SK ausgeliefert werden.








