Nzeru zanu zimasonyeza mmene mumaganizira. Nzeru zimakupangani kukhala munthu wothandiza. Munthu wanzeru amamanga kanthu. Zimene mwamanga zimasonyeza nzeru zanu. Nzeru ndiye chinsinsi chautsogoleri chomwe mungafune pautumiki. Nzeru ndiye chinsinsi chothana ndi zovuta za utsogoleri.
Solomo anapempha nzeru kwa Mulungu. Mulungu anam'patsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu. Chotsatira cha mtima wanzeru ndi wozindikira umenewu chimawonekera m'Baibulo lonse.
Bukhuli silinena za kuchenjera kwa anthu kapena zolankhula zonyenga. Bukhuli silikunena za mawu omveka bwino omwe amagwiritsidwa ntchito kusokoneza anthu.
Mlembi, Bishopu Dag Heward-Mills, amafuna kuunikira owerenga kuti ngakhale pali mitundu yosiyanasiyana ya nzeru, mawu a Mulungu ndiwo apambana.
Dieser Download kann aus rechtlichen Gründen nur mit Rechnungsadresse in A, B, CY, CZ, D, DK, EW, E, FIN, F, GR, H, IRL, I, LT, L, LR, M, NL, PL, P, R, S, SLO, SK ausgeliefert werden.








